Salimo 73:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anena kuti: “Mulungu angadziwe bwanji?+Kodi Wam’mwambamwamba akudziwa zimenezi?”+ Yesaya 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsoka kwa anthu amene abisa patali kwambiri zolinga zawo, pozibisira Yehova,+ amene zochita zawo zimachitikira m’malo a mdima,+ ndipo amati: “Ndani akutiona, ndipo ndani akudziwa zimene tikuchita?”+
15 Tsoka kwa anthu amene abisa patali kwambiri zolinga zawo, pozibisira Yehova,+ amene zochita zawo zimachitikira m’malo a mdima,+ ndipo amati: “Ndani akutiona, ndipo ndani akudziwa zimene tikuchita?”+