Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+

      Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+

  • Salimo 37:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova amadziwa za moyo wa anthu osalakwa,+

      Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Salimo 112:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 112 Tamandani Ya, anthu inu!+

      א [ʼAʹleph]

      Wodala ndi munthu woopa Yehova,+

      ב [Behth]

      Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+

  • Salimo 115:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova adzadalitsa anthu omuopa,+

      Adzadalitsa onsewo osasiyapo aliyense.+

  • Yesaya 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+

  • Yesaya 65:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya,+ koma inuyo mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inuyo mudzakhala ndi ludzu.+ Atumiki anga adzasangalala,+ koma inuyo mudzachita manyazi.+

  • Mateyu 25:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+

  • 2 Petulo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena