Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+

      Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+

  • Salimo 119:165
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 165 Okonda chilamulo chanu amapeza mtendere wochuluka,+

      Ndipo palibe chowakhumudwitsa.+

  • Yesaya 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu amene ali ndi mtima wosagwedezeka mudzawateteza powapatsa mtendere wosatha,+ chifukwa amadalira inu.+

  • Yesaya 48:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+

  • Afilipi 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena