Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+ Amosi 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera pamene ndidzatumiza njala m’dziko. Njala imeneyo siidzakhala ya chakudya kapenanso ludzu lofuna madzi ayi, koma idzakhala njala ndiponso ludzu lofuna kumva mawu a Yehova.+
11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera pamene ndidzatumiza njala m’dziko. Njala imeneyo siidzakhala ya chakudya kapenanso ludzu lofuna madzi ayi, koma idzakhala njala ndiponso ludzu lofuna kumva mawu a Yehova.+