Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zili choncho, mwanayo Samueli anali kutumikira+ Yehova pamaso pa Eli, ndipo mawu a Yehova+ anali osowa masiku amenewo,+ moti masomphenya sanali kuonekaoneka.+

  • Salimo 74:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Zizindikiro zathu sitinazione, ndipo palibenso mneneri amene watsala,+

      Pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zikhala choncho mpaka liti.

  • Ezekieli 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 M’dzikolo mudzakhala mavuto otsatizanatsatizana+ ndipo muzidzamveka mauthenga otsatizanatsatizana. Anthu azidzafunafuna masomphenya kwa mneneri.+ Ansembe sadzathanso kuphunzitsa malamulo aphindu. Anthu achikulire sadzaperekanso malangizo othandiza.+

  • Mateyu 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena