1 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zili choncho, mwanayo Samueli anali kutumikira+ Yehova pamaso pa Eli, ndipo mawu a Yehova+ anali osowa masiku amenewo,+ moti masomphenya sanali kuonekaoneka.+ Amosi 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera pamene ndidzatumiza njala m’dziko. Njala imeneyo siidzakhala ya chakudya kapenanso ludzu lofuna madzi ayi, koma idzakhala njala ndiponso ludzu lofuna kumva mawu a Yehova.+
3 Zili choncho, mwanayo Samueli anali kutumikira+ Yehova pamaso pa Eli, ndipo mawu a Yehova+ anali osowa masiku amenewo,+ moti masomphenya sanali kuonekaoneka.+
11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera pamene ndidzatumiza njala m’dziko. Njala imeneyo siidzakhala ya chakudya kapenanso ludzu lofuna madzi ayi, koma idzakhala njala ndiponso ludzu lofuna kumva mawu a Yehova.+