Amosi 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubweraPamene ndidzatumiza njala mʼdziko.Osati njala ya chakudya kapena ludzu lofuna madzi,Koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:11 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 255/1/2004, ptsa. 16-177/1/1998, tsa. 3
11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubweraPamene ndidzatumiza njala mʼdziko.Osati njala ya chakudya kapena ludzu lofuna madzi,Koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.+