Numeri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+ 1 Mbiri 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Natani anauza Davide mawu onsewa ndi masomphenya onse amene anaona.+
6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+