Genesis 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene ziweto zinali m’nthawi yotentha thupi kukonzekera kutenga bere, ndinakweza maso anga n’kuona m’maloto+ mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+ Yeremiya 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova.
10 Pamene ziweto zinali m’nthawi yotentha thupi kukonzekera kutenga bere, ndinakweza maso anga n’kuona m’maloto+ mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+
28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova.