Miyambo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yokhulupirika ndi imene sinama,+ koma mboni yonyenga imanena bodza lokhalokha.+ Luka 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+ 2 Akorinto 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ifeyo ndife oyenerera. Pakuti mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri akuchitira,+ koma timalankhula moona mtima monga otsatira Khristu, okhala pamaso pa Mulungu, komanso ngati anthu amene atumidwa ndi Mulungu.+
42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+
17 Ifeyo ndife oyenerera. Pakuti mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri akuchitira,+ koma timalankhula moona mtima monga otsatira Khristu, okhala pamaso pa Mulungu, komanso ngati anthu amene atumidwa ndi Mulungu.+