Miyambo 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wotulutsa mawu okhulupirika amanena zolungama,+ koma mboni yonama imanena zachinyengo.+ 2 Akorinto 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 olankhula zoona, ndiponso okhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso, tikuchita zimenezi ponyamula zida+ za chilungamo kudzanja lamanja ndi lamanzere,
7 olankhula zoona, ndiponso okhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso, tikuchita zimenezi ponyamula zida+ za chilungamo kudzanja lamanja ndi lamanzere,