2 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti zida za nkhondo yathu si zochokera m’dziko lino,+ koma ndi zida zamphamvu zimene Mulungu watipatsa,+ zimene zimatha kugwetsa zinthu zozikika molimba. Aefeso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,
4 Pakuti zida za nkhondo yathu si zochokera m’dziko lino,+ koma ndi zida zamphamvu zimene Mulungu watipatsa,+ zimene zimatha kugwetsa zinthu zozikika molimba.
11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,