Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Bwezera lupanga lako m’chimake,+ pakuti onse ogwira lupanga adzafa ndi lupanga.+

  • Aroma 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+

  • Aefeso 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa chifukwa chimenechi, nyamulani zida zonse zankhondo zochokera kwa Mulungu+ kuti musadzagonje m’tsiku loipa, ndipo mutachita zonse bwinobwino, mudzathe kulimba.+

  • 1 Atesalonika 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ife amene tili a usana, tikhalebe oganiza bwino ndipo tivale chodzitetezera pachifuwa+ chachikhulupiriro+ ndi chikondi. Tivalenso chiyembekezo chachipulumutso+ monga chisoti,+

  • 1 Timoteyo 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mwana wanga Timoteyo, ndikukulamulira+ kuchita izi malinga ndi maulosi+ amene ananeneratu za iwe, kuti mogwirizana ndi maulosiwo upitirize kumenya nkhondo yabwino.+

  • 2 Timoteyo 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena