Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Chivumbulutso 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati wina akuyenera kutengedwa ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko.+ Ngati wina adzapha ndi lupanga, adzaphedwa ndi lupanga.+ Apa m’pamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
10 Ngati wina akuyenera kutengedwa ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko.+ Ngati wina adzapha ndi lupanga, adzaphedwa ndi lupanga.+ Apa m’pamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+