Danieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma oyera+ a Wamkulukulu+ adzalandira ufumu ndipo adzatenga ufumuwo+ mpaka kalekale, ku nthawi zosatha.’ 1 Akorinto 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kapena simukudziwa kuti oyerawo adzaweruza+ dziko?+ Ndipo ngati mudzaweruza dziko, kodi simungathe kuzenga milandu yaing’ono kwambiri+ ngati imeneyo? Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+
18 Koma oyera+ a Wamkulukulu+ adzalandira ufumu ndipo adzatenga ufumuwo+ mpaka kalekale, ku nthawi zosatha.’
2 Kapena simukudziwa kuti oyerawo adzaweruza+ dziko?+ Ndipo ngati mudzaweruza dziko, kodi simungathe kuzenga milandu yaing’ono kwambiri+ ngati imeneyo?
6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+