Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosangalala komanso woyera ndi aliyense amene akuuka nawo pa kuuka koyamba.+ Imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro pa amenewa.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu zaka 1,000.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 290-291 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, ptsa. 11-12 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 172-173
6 Wosangalala komanso woyera ndi aliyense amene akuuka nawo pa kuuka koyamba.+ Imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro pa amenewa.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu zaka 1,000.+
20:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 290-291 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, ptsa. 11-12 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 172-173