Chivumbulutso 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Amene ali ndi makutu amve+ zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti: Amene wapambana pankhondo+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+ Chivumbulutso 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo imfa ndi Manda* zinaponyedwa mʼnyanja yamoto.+ Nyanja yamoto+ imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+
11 Amene ali ndi makutu amve+ zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti: Amene wapambana pankhondo+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+
14 Ndipo imfa ndi Manda* zinaponyedwa mʼnyanja yamoto.+ Nyanja yamoto+ imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+