Chivumbulutso 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ali ndi makutu amve+ zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 28-29, 38-39
11 Ali ndi makutu amve+ zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+