Chivumbulutso 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Amene ali ndi makutu amve+ zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti: Amene wapambana pankhondo+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 28-29, 38-39
11 Amene ali ndi makutu amve+ zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti: Amene wapambana pankhondo+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+