13 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba akuti, “Lemba kuti: Osangalala ndi anthu amene akufa ali ogwirizana ndi Ambuye+ kuyambira pa nthawi ino kupita mʼtsogolo. Mzimu ukuti asiyeni apume ku ntchito yawo imene anaigwira mwakhama, chifukwa zimene anachita zikupita nawo limodzi.”