Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15:51, 52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Tamverani, ndikuuzeni chinsinsi chopatulika: Sikuti tonse tidzagona mu imfa, koma tonse tidzasintha,+ 52 mʼkanthawi kochepa, mʼkuphethira kwa diso, pa kulira kwa lipenga lomaliza. Chifukwa lipenga lidzalira,+ kenako akufa adzaukitsidwa ndi matupi oti sangawonongeke ndipo tidzasintha.

  • 1 Atesalonika 4:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa Ambuyewo adzatsika kuchoka kumwamba ndi mfuu yolamula. Mawu awo adzamveka kuti ndi a mkulu wa angelo+ ndipo adzanyamula lipenga la Mulungu mʼdzanja lawo. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka.+ 17 Pambuyo pake ife amene tidzakhale tidakali ndi moyo, limodzi ndi iwowo, tidzatengedwa kupita mʼmitambo+ kukakumana ndi Ambuye+ mumlengalenga ndipo tizikakhala ndi Ambuye nthawi zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena