Yuda 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pamene Mikayeli,+ mkulu wa angelo,+ anasemphana maganizo ndi Mdyerekezi ndipo anakangana naye za mtembo wa Mose,+ sanayese nʼkomwe kumuweruza komanso kumunyoza,+ mʼmalomwake anati: “Yehova* akudzudzule.”+
9 Koma pamene Mikayeli,+ mkulu wa angelo,+ anasemphana maganizo ndi Mdyerekezi ndipo anakangana naye za mtembo wa Mose,+ sanayese nʼkomwe kumuweruza komanso kumunyoza,+ mʼmalomwake anati: “Yehova* akudzudzule.”+