Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+ Chivumbulutso 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ali ndi makutu amve+ zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+ Chivumbulutso 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo imfa+ ndi Manda zinaponyedwa m’nyanja yamoto.+ Nyanja yamoto imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
11 Ali ndi makutu amve+ zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ sadzakhudzidwa ndi imfa yachiwiri.’+
14 Ndipo imfa+ ndi Manda zinaponyedwa m’nyanja yamoto.+ Nyanja yamoto imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+