1 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Ndani pakati pa atumiki anu onse ali ngati Davide,+ munthu wokhulupirika,+ mkamwini+ wa mfumu, mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka m’nyumba yanu?+
14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Ndani pakati pa atumiki anu onse ali ngati Davide,+ munthu wokhulupirika,+ mkamwini+ wa mfumu, mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka m’nyumba yanu?+