1 Samueli 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero Yonatani analankhula zabwino+ za Davide kwa Sauli bambo ake, kuti: “Mfumu isachimwire+ mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakuchimwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.+ 1 Samueli 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma Yonatani anayankha Sauli bambo ake kuti: “Aphedwe chifukwa chiyani?+ Walakwanji?”+
4 Chotero Yonatani analankhula zabwino+ za Davide kwa Sauli bambo ake, kuti: “Mfumu isachimwire+ mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakuchimwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.+