Salimo 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga amandibwezera zoipa m’malo mwa zabwino,+Ndipo ndimakhala wachisoni ngati wofedwa.+ Salimo 109:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikawachitira zabwino amandibwezera zoipa,+Ndikawasonyeza chikondi amandibwezera chidani.+ Miyambo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense wobwezera zoipa pa zabwino,+ zoipa sizidzachoka panyumba pake.+ Yeremiya 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+
20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+