Salimo 106:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+ Ezekieli 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala+ ndi kuima pamalo ogumuka a mpandawo+ kuti ateteze dzikolo n’cholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense.
23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+
30 “‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala+ ndi kuima pamalo ogumuka a mpandawo+ kuti ateteze dzikolo n’cholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense.