Genesis 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Abulahamu anamuyandikira n’kuyamba kumufunsa kuti: “Kodi zoona mungawononge olungama pamodzi ndi oipa?+ Ekisodo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Mose anakhazika pansi mtima wa Yehova Mulungu wake.+ Iye anati: “N’chifukwa chiyani, inu Yehova, mukufuna kuti mkwiyo wanu+ uyakire anthu anu, amene munawatulutsa m’dziko la Iguputo mwa mphamvu zazikulu ndiponso ndi dzanja lamphamvu?
23 Ndiyeno Abulahamu anamuyandikira n’kuyamba kumufunsa kuti: “Kodi zoona mungawononge olungama pamodzi ndi oipa?+
11 Pamenepo Mose anakhazika pansi mtima wa Yehova Mulungu wake.+ Iye anati: “N’chifukwa chiyani, inu Yehova, mukufuna kuti mkwiyo wanu+ uyakire anthu anu, amene munawatulutsa m’dziko la Iguputo mwa mphamvu zazikulu ndiponso ndi dzanja lamphamvu?