Genesis 42:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Rubeni anayankhira kuti: “Kodi ine sindinanene kuti, ‘Mwanayu musam’chite choipa’? Koma inu simunamve.+ Si izi nanga, magazi ake akufunidwatu kwa ife.”+ 2 Mbiri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+ 1 Yohane 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene amadana+ ndi m’bale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu+ sadzalandira moyo wosatha.+
22 Ndiyeno Rubeni anayankhira kuti: “Kodi ine sindinanene kuti, ‘Mwanayu musam’chite choipa’? Koma inu simunamve.+ Si izi nanga, magazi ake akufunidwatu kwa ife.”+
23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+
15 Aliyense amene amadana+ ndi m’bale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu+ sadzalandira moyo wosatha.+