Genesis 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Rubeni atamva zimenezo anayesa kum’landitsa kwa iwo.+ Iye anati: “Ayi, tisachite kuwononga moyo wake.”+ Aroma 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amenewa ndiwo amasonyeza kuti mfundo za m’chilamulo zinalembedwa m’mitima mwawo,+ pamene chikumbumtima chawo+ chimachitira umboni pamodzi ndi iwowo, ndipo maganizo awo amawatsutsa+ ngakhalenso kuwavomereza.
21 Rubeni atamva zimenezo anayesa kum’landitsa kwa iwo.+ Iye anati: “Ayi, tisachite kuwononga moyo wake.”+
15 Amenewa ndiwo amasonyeza kuti mfundo za m’chilamulo zinalembedwa m’mitima mwawo,+ pamene chikumbumtima chawo+ chimachitira umboni pamodzi ndi iwowo, ndipo maganizo awo amawatsutsa+ ngakhalenso kuwavomereza.