2 Mbiri 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pomalizira pake ansembe achilevi anaimirira n’kudalitsa+ anthuwo, ndipo mawu awo anamvedwa moti pemphero lawo linafika kumwamba, kumalo oyera okhala Mulungu.+ Salimo 123:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Ndakweza maso anga kuyang’ana inu,+Kuyang’ana inu amene mukukhala kumwamba.+
27 Pomalizira pake ansembe achilevi anaimirira n’kudalitsa+ anthuwo, ndipo mawu awo anamvedwa moti pemphero lawo linafika kumwamba, kumalo oyera okhala Mulungu.+