Salimo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+ Salimo 121:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 121 Ndakweza maso anga kuyang’ana kumapiri.+Kodi thandizo langa lichokera kuti?+ Salimo 141:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ine maso anga ali pa inu+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndathawira kwa inu.+Musalole kuti moyo wanga uwonongeke.+ Luka 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma wokhometsa msonkho uja, ataima chapatali ndithu, sanafune ngakhale kukweza maso ake kumwamba. Anali kungodziguguda pachifuwa+ ndi kunena kuti, ‘Mulungu wanga, ndikomereni mtima munthu wochimwa ine.’+
15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+
8 Koma ine maso anga ali pa inu+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndathawira kwa inu.+Musalole kuti moyo wanga uwonongeke.+
13 Koma wokhometsa msonkho uja, ataima chapatali ndithu, sanafune ngakhale kukweza maso ake kumwamba. Anali kungodziguguda pachifuwa+ ndi kunena kuti, ‘Mulungu wanga, ndikomereni mtima munthu wochimwa ine.’+