Salimo 121:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 121 Ndakweza maso anga kuyang’ana kumapiri.+Kodi thandizo langa lichokera kuti?+ Salimo 123:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Ndakweza maso anga kuyang’ana inu,+Kuyang’ana inu amene mukukhala kumwamba.+ Salimo 141:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ine maso anga ali pa inu+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndathawira kwa inu.+Musalole kuti moyo wanga uwonongeke.+
8 Koma ine maso anga ali pa inu+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndathawira kwa inu.+Musalole kuti moyo wanga uwonongeke.+