Salimo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+ Salimo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+ Salimo 71:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Inu Yehova, ine ndathawira kwa inu.+Musalole kuti ndichite manyazi.+
11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+
11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+