Salimo 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lemekezani Yehova pamodzi ndi ine+ anthu inu,Tiyeni tonse tikweze dzina lake.+ Salimo 69:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ana a atumiki ake adzalandira dzikolo monga cholowa chawo,+Ndipo anthu okonda dzina lake adzakhala mmenemo.+
36 Ana a atumiki ake adzalandira dzikolo monga cholowa chawo,+Ndipo anthu okonda dzina lake adzakhala mmenemo.+