Salimo 102:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana a atumiki anu adzapitiriza kukhala motetezeka pamaso panu.+Ndipo ana awo adzakhazikika pamaso panu.”+ Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+ Yesaya 66:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pakuti monga momwe kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzakhalirebe pamaso panga,+ momwemonso ana anu+ ndi dzina lanu zidzakhalapo mpaka kalekale,”+ akutero Yehova.
28 Ana a atumiki anu adzapitiriza kukhala motetezeka pamaso panu.+Ndipo ana awo adzakhazikika pamaso panu.”+
9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+
22 “Pakuti monga momwe kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzakhalirebe pamaso panga,+ momwemonso ana anu+ ndi dzina lanu zidzakhalapo mpaka kalekale,”+ akutero Yehova.