Genesis 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+ Zekariya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Monga mmene munakhalira temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a nyumba ya Yuda ndi a nyumba ya Isiraeli,+ ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo mukonzeke kugwira ntchito.’+
18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+
13 Monga mmene munakhalira temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a nyumba ya Yuda ndi a nyumba ya Isiraeli,+ ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo mukonzeke kugwira ntchito.’+