Zekariya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Popeza munali temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a mʼnyumba ya Yuda ndi a mʼnyumba ya Isiraeli ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Limbani mtima,+ musachite mantha.’+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 19
13 Popeza munali temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a mʼnyumba ya Yuda ndi a mʼnyumba ya Isiraeli ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Limbani mtima,+ musachite mantha.’+