-
Yesaya 19:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Pa tsiku limenelo, anthu a ku Isiraeli adzakhala gulu lachitatu, ataphatikizana ndi Aiguputo komanso Asuri,+ amenewa adzakhala madalitso padziko lapansi, 25 chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzakhala atawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Adalitsike Aiguputo anthu anga, Asuri ntchito ya manja anga komanso Aisiraeli omwe ndi cholowa changa.”+
-