2 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+
18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+