Deuteronomo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale ku Horebe, inu munaputa mkwiyo wa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Deuteronomo 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova sadzafuna kukhululukira+ munthu woteroyo, m’malomwake mkwiyo+ ndi ukali+ wa Yehova udzamuyakira,+ ndipo matemberero onse olembedwa m’buku+ ili adzakhala pa iye, motero Yehova adzafafanizadi dzina la munthuyo pansi pa thambo. 1 Mafumu 8:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+
8 Ngakhale ku Horebe, inu munaputa mkwiyo wa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+
20 Yehova sadzafuna kukhululukira+ munthu woteroyo, m’malomwake mkwiyo+ ndi ukali+ wa Yehova udzamuyakira,+ ndipo matemberero onse olembedwa m’buku+ ili adzakhala pa iye, motero Yehova adzafafanizadi dzina la munthuyo pansi pa thambo.
46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+