Ekisodo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+ Salimo 79:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+ Ezekieli 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzasonyeza ukali wanga pa iwe+ ndipo iwo adzakulanga mwaukali.+ Adzakuchotsa mphuno ndi makutu ndipo ziwalo zako zotsala adzazidula ndi lupanga. Iwo adzatenga+ ana ako aamuna ndi aakazi+ ndipo zinthu zako zotsala adzazitentha ndi moto.+
14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+
5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+
25 Ndidzasonyeza ukali wanga pa iwe+ ndipo iwo adzakulanga mwaukali.+ Adzakuchotsa mphuno ndi makutu ndipo ziwalo zako zotsala adzazidula ndi lupanga. Iwo adzatenga+ ana ako aamuna ndi aakazi+ ndipo zinthu zako zotsala adzazitentha ndi moto.+