Deuteronomo 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova sadzafuna kukhululukira+ munthu woteroyo, m’malomwake mkwiyo+ ndi ukali+ wa Yehova udzamuyakira,+ ndipo matemberero onse olembedwa m’buku+ ili adzakhala pa iye, motero Yehova adzafafanizadi dzina la munthuyo pansi pa thambo. Ezekieli 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+ Zefaniya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Moto wa mkwiyo wake udzanyeketsa dziko lonse lapansi,+ chifukwa iye adzafafaniza anthu onse okhala padziko lapansi.”+
20 Yehova sadzafuna kukhululukira+ munthu woteroyo, m’malomwake mkwiyo+ ndi ukali+ wa Yehova udzamuyakira,+ ndipo matemberero onse olembedwa m’buku+ ili adzakhala pa iye, motero Yehova adzafafanizadi dzina la munthuyo pansi pa thambo.
19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+
18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Moto wa mkwiyo wake udzanyeketsa dziko lonse lapansi,+ chifukwa iye adzafafaniza anthu onse okhala padziko lapansi.”+