Ezekieli 16:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “‘Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimaperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi,+ ndipo ndidzakupatsa magazi a mkwiyo ndi nsanje.+
38 “‘Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimaperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi,+ ndipo ndidzakupatsa magazi a mkwiyo ndi nsanje.+