Ezekieli 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzasonyeza ukali wanga pa iwe+ ndipo iwo adzakulanga mwaukali.+ Adzakuchotsa mphuno ndi makutu ndipo ziwalo zako zotsala adzazidula ndi lupanga. Iwo adzatenga+ ana ako aamuna ndi aakazi+ ndipo zinthu zako zotsala adzazitentha ndi moto.+ Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+ Zefaniya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ndidzasautsa mtundu wa anthu moti adzayenda ngati anthu akhungu+ chifukwa chakuti iwo achimwira Yehova.+ Magazi awo adzakhuthulidwa pansi ngati fumbi,+ ndipo matumbo awo adzakhuthulidwa pansi ngati ndowe.+
25 Ndidzasonyeza ukali wanga pa iwe+ ndipo iwo adzakulanga mwaukali.+ Adzakuchotsa mphuno ndi makutu ndipo ziwalo zako zotsala adzazidula ndi lupanga. Iwo adzatenga+ ana ako aamuna ndi aakazi+ ndipo zinthu zako zotsala adzazitentha ndi moto.+
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
17 Pamenepo ndidzasautsa mtundu wa anthu moti adzayenda ngati anthu akhungu+ chifukwa chakuti iwo achimwira Yehova.+ Magazi awo adzakhuthulidwa pansi ngati fumbi,+ ndipo matumbo awo adzakhuthulidwa pansi ngati ndowe.+