Yesaya 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+ chifukwa alambalala malamulo,+ asintha malamulowo+ ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.+ Danieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+
5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+ chifukwa alambalala malamulo,+ asintha malamulowo+ ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.+
5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+