Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+ Yeremiya 31:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Koma pangano limeneli si lofanana ndi limene ndinapangana ndi makolo awo pamene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse m’dziko la Iguputo.+ ‘Pangano langa limenelo analiphwanya+ ngakhale kuti ine ndinali mwamuna wawo,’+ watero Yehova.” Yeremiya 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amene akupatuka pa pangano langa+ mwa kusatsatira mawu a m’pangano limene iwo anachita pamaso panga, ndidzawapereka kwa adani. Iwo anachita pangano limeneli mwakudula pakati+ mwana wa ng’ombe wamphongo ndi kudutsa pakati pake.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+
32 “Koma pangano limeneli si lofanana ndi limene ndinapangana ndi makolo awo pamene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse m’dziko la Iguputo.+ ‘Pangano langa limenelo analiphwanya+ ngakhale kuti ine ndinali mwamuna wawo,’+ watero Yehova.”
18 Anthu amene akupatuka pa pangano langa+ mwa kusatsatira mawu a m’pangano limene iwo anachita pamaso panga, ndidzawapereka kwa adani. Iwo anachita pangano limeneli mwakudula pakati+ mwana wa ng’ombe wamphongo ndi kudutsa pakati pake.+