Yeremiya 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo izi ndi zimene zidzachitikire anthu amene anaphwanya pangano langa posatsatira mawu a mʼpangano limene iwo anachita pamaso panga. Iwo anachita pangano limeneli podula mwana wa ngʼombe pakati nʼkudutsa pakati pa mbali ziwirizo.+
18 Ndipo izi ndi zimene zidzachitikire anthu amene anaphwanya pangano langa posatsatira mawu a mʼpangano limene iwo anachita pamaso panga. Iwo anachita pangano limeneli podula mwana wa ngʼombe pakati nʼkudutsa pakati pa mbali ziwirizo.+