Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 komanso m’chipululu,+ kumene munaona mmene Yehova Mulungu wanu anakunyamulirani.+ M’njira yonse imene munayenda anakunyamulani ngati mmene bambo amanyamulira mwana wake, mpaka kufika malo ano.’+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
31 komanso m’chipululu,+ kumene munaona mmene Yehova Mulungu wanu anakunyamulirani.+ M’njira yonse imene munayenda anakunyamulani ngati mmene bambo amanyamulira mwana wake, mpaka kufika malo ano.’+