Salimo 78:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anang’amba miyala m’chipululu+Kuti awapatse madzi akumwa ochuluka ngati a m’nyanja.+